Police station yotithandiza kulibe

12-Apr-2016 | 13:29

Kwathu kuno katundu akubedwa.. anthu akuphedwa paliibe chabwino kukacha timamva nkhani za chisoni ........ a MP anthu tinawafotokozela kuti kuta khala police station bola tithandizika....... anangoti amva

security

12-May-2016 | 10:23

Here in area 47 lilongwe,we need another police unit close by, the one at Gateway mall is far

Kuthokoza Chi 2 Ward

25-Jul-2016 | 10:41

Tikuthoza a Cllr Kamtondoli a Chi 2 ward poyamba chitukuko cha Police mdera lawo

Security Concern Mchesi Ward

08-Aug-2016 | 16:30

Mchesi we need a police unit. It seems the same pple entrusted wt community policing are thieves. Concerned Businessman

Chitetezo Kwa Mgona

12-Aug-2016 | 09:40

mwa mgona mwachuluka umbava. Khansala akambe ndi apolisi. ya community sikuthandiza

Atipatse Police Unit ku Mtandile

19-Aug-2016 | 20:46

Vuto lina tili nalo ku Mtandile ndikuchepa kwa Chitetezo. Atipatse Police Unit ngati kuli kotheka. Felix Chikopa

Mavuto Aku Mtandile

19-Aug-2016 | 12:03

Kuno ku mtandile timakumana ndi mavuto akusowa kwamadzi,magetsi,misewu yamakono,police unit.

Kuyamikira Community Police Ya kwa Biwi

09-Sep-2016 | 03:15

Tiyamikire community police kwa biwi zilibwino

Efforts Being Made By Police Patrols

15-Sep-2016 | 06:55

Taken note of more Police patrols around town. good considering the danger criminals pose

Tiyamikire Khansala wathu Nyama ward

17-Oct-2016 | 07:58

ndati ndiyamike kuti khansala wathu wa Nyama ward ntchito akuigwira. Chilimbikitso chawo pa Community police chakhwimitsa chitetezo kuno

Tili pa Chiophyezo kuno ku Chikwawa

13-Dec-2016 | 10:45

Ndati ndidandaule kui kuno ku Chikwawa tili pa chiophyezo chifukwa pa police unit yathu pano mwezi ukutha popanda anthu. omwe adalipo tidamva kuti adawapanga transfer koma olowa m'malo mwao sadabwere mpaka lero

Pempho pa nkhani ya chitetezo ku Area 36

17-Mar-2017 | 17:28

Kuno ku Area 36 m’maka ma dera akwa Zapita ndi Kandikole umbava ukuchuluka. Tipemphe atsogoleri athu alinganize ndi a community police achitepo kanthu