Magetsi khatabay

12-Apr-2016 | 12:35

Kwathu kuno magetsi sakuyaka tikutha 1 week pano wopanda magetsi kuwauza a-Escom faults anangoti amva pali vuto la transformer.

Magetsi akuvuta kuno

21-Jul-2016 | 11:25

Kuno ku ndilande golio mangetsi akuvuta kwambiri

Magesi Kuno

02-Aug-2016 | 14:07

kumasasa kunyake magesi kulije nga ku kanthete wasambizi wakuchimbirako chifukwa cha ichi

MAGETSI AKUVUTA

05-Aug-2016 | 15:01

Area 25C magetsi akuvuta kwambiri

Madzi ndi Magetsi

08-Aug-2016 | 17:35

Geisha ku Masasa Ward tilibe madzi abwino ine ngati mwanakazi nkhusuzgika kutheka madgi komanso magetsi tikuvutika ngati siku city.

Kuzimazima kwa Magetsi *Resolved*

16-Aug-2016 | 17:17

Kuno ku likuni magetsi amangothimathima.. tikupempha kuti ESCOM iunikepo chifukwa kulekana ndi madera ena ife akathima pamatenga nthawi kuti ayakenso

Electricity Concern Likuni *Resolved*

18-Aug-2016 | 21:11

Likuni we are having problems of Electricity, as much as we understand the Load shedding program koma kuno kuthima thima kwayenjeza

Kuno ku Area 18 magetsi ndi madzi akuvuta

18-Aug-2016 | 13:30

Magesi ndi madzi akumavuta kuno ku Area 18

Kodi tingadziwe bwanji zakuzima kwa magesi?

23-Aug-2016 | 11:32

Ndati ndifunseko nawo kuti kodi tingathe kudziwa bwanji kuti magetsi azima komanso kuyaka nyengo yanji?

Magesi Akuvuta Area 49 Gulliver

18-Aug-2016 | 13:53

Magetsi akuvuta angozimazima kuno ku area 49 Gulliver

Magesi kwa Senti

18-Aug-2016 | 13:51

kuno kwa senti magesi ndi vuto, aunike bwino ma line podula-nkuyatsa tumakhala nyengo yaitali mu mdima

Vuto la Magetsi

02-Aug-2016 | 14:01

magetsi akumazimazima kuno kwa senti