Hate Speech During Debates

19-Apr-2019 | 22:04

There was a political debate at Nkhwangwa CDSS that ended abruplty after hate speech exchanged between DPP and MCP supporters

Chisankho Chaima Kaye Kuno *Resolved*

21-May-2019 | 17:44

Chisankho chaima kaye pa Phaka school, Chongoni ward in Dedza Central East zikuoneka ngati chifukwa panali kusamvana panabwera anthu ena ake atatu amati ndi ma roving monitors achipani