LAND GIVEN ILLEGALY

08-Aug-2016 | 10:10

Government land has been given to people illegally in my area, Chisapo 2

magetsi amu nsewu

12-Apr-2016 | 13:04

Kwathu kuno mbali mwa nseu mulibe magetsi a MP anthu tinawauza koma mpaka lero sakuchitapo kathu

Malo amsika ku Geisha

02-Aug-2016 | 14:40

Ku Geisha masasa ward msika uli m'mbali mwa nseu tikufuna uchoke kupewa ngozi

PEMPHO

06-Aug-2016 | 10:10

ine ngati khansala wa Tsabango 2 ward tikupempha anthu akufuna kwabwino atithandizire pa zitukuko zomwe tayambapo kale chifukwa tikuperedwa mbali zina. Ofuna kwabwino mukhoza kulankhula nafe pa nambali izi +265 999 73 35 31 / 888 56 27 30

MALO YAMSIKA *Resolved*

07-Aug-2016 | 03:14

tikulutilira kupempha muwaphalireko ku city va msika wa Geisha wadumbisane na mwenecho wa malo kuti wathu tambepo kuzenga

Malo Amsika Sali Bwino

08-Aug-2016 | 17:35

Pa Geisha msika uchotsedwe ndipoyipa ndimmbali mwamseu ngozi zikuchuluka ufunika pa malo abwino otakasuka

MZINDA MCHICHEWA

12-Aug-2016 | 06:30

Good platform. For sure this will keep our leaders and service providers on the alert and so we can hold them accountable. But wouldn't there be an option like the way it is with phones kuti ena can view the platform in CHICHEWA

Tikupempha nawo Admarc kwa Mtsiliza

17-Aug-2016 | 12:13

Kuno kwa mtsiliza kulibe Admarc yokhazikika tingatani kuti anthu asamakagone ku Maula Admarc?

Khansala wa dera langa sindimudziwa

22-Aug-2016 | 20:52

Khansala wa dera limene ndikukhala sindikumudziwa thandizeni. kwa Phwetekere

Tikufuna Bank kwa Mtsiliza

21-Jul-2016 | 09:19

GETO INO TIMASOWA BANK; Kodi Ife Kwamtsiliza Kno Sitifunika Kukhala Ndi Bank? Ndine MD Signwriter

Tiyamikire Mzinda

21-Aug-2016 | 15:13

zikomo kwambiri a-Mzinda chifukwa chopereka mwayi woti titha kumalemba ma uthenga pa mavuto akudera

Chitukuko kuno ku Nankhaka

01-Sep-2016 | 07:20

Kuno ku NANKHAKA WARD Tikukumba Dam under MASAF 4 LDF project. Tiweta nsomba ndi kulima mbeu zanthilira.Timafuna mutabwela pa 2/09/16 pamwambo woyamba ntchito imeneyi. Nankhaka ward Cllr WILBES KAPIZA