Verified

  • 12-Apr-2016 | 13:28

chipatala kulibe pafupi

kuno kwathu ku Chiradzulu kwa pelembe dera lonse kuchoka mbali ya kwa mpama kulibe chipatala tikadwala timayenda kukafika ku chipatala chachikulu

Location